Yesaya 22:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Katundu wa cigwa ca masomphenya.Mwatani kuti mwakwera nonsenu pamacindwi?

2. Iwe amene wadzala ndi zimpfuu, mudzi waphokoso, mudzi wokondwa; ophedwa ako, sanaphedwa ndi lupanga, sanafe m'nkhondo.

Yesaya 22