Yesaya 17:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ku Efraimu sikudzakhalanso linga, ngakhale ufumu ku Damasiko, ngakhale otsala kwa Aramu; iwo adzakhala ngati ulemerero wa ana a Israyeli, ati Yehova wamakamu.

Yesaya 17

Yesaya 17:1-7