Yesaya 16:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mpando wacifumu udzakhazikika m'cifundo, ndimo wina adzakhala pamenepo m'zoona, m'cihema ca Davide, nadzaweruza, nadzafunitsa ciweruziro, nadzafulumira kucita cilungamo.

Yesaya 16

Yesaya 16:1-13