Yeremiya 7:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzakukhazikani inu m'malo muno, m'dziko limene ndinapatsa makolo anu, kuyambira kale lomwe kufikira muyaya,

Yeremiya 7

Yeremiya 7:1-14