Yeremiya 51:63-64 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

63. Ndipo padzakhala, utatha kuwerenga buku ili, Ib ulimange ndi mwala, nuliponye pakati pa Firate;

64. nuti, Comweco adzamira Babulo, sadzaukanso cifukwa ca coipa cimene ndidzamtengera iye; ndipo adzatopa.Mau a Yeremiya ndi omwewo.

Yeremiya 51