Yeremiya 51:62 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nuti, inu Yehova, mwanena za malo ano, kuti mudzawatha, kuti asakhalemo, ngakhale anthu ngakhale nyama, koma akhale bwinja nthawi za nthawi.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:56-64