Yeremiya 51:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, taona, masiku alinkudza, ati Yehova, amene ndidzaweruza mafano ace; ndipo pa dziko lace lonse olasidwa adzabuula.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:49-58