Yeremiya 51:39-42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Pamene atentha, ndidzakonza madyerero ao, ndidzawaledzeretsa, kuti asangalale, agone cigonere, asanyamuke, ati Yehova.

40. Ndidzawagwetsa kuti aphedwe manga nkhosa zamphongo, ndi atonde.

41. Sesake wagwidwatul cimene dziko lonse lapansi linacitamanda calandidwa dzidzidzi Babulo wakhalatu bwinja pakati pa amitundu

42. Nyanja yakwera kufikira ku Babulo; wamira ndi mafunde ace aunyinji.

Yeremiya 51