Yeremiya 51:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Olimba a ku Babulo akana kumenyana, akhala m'malinga ao; mphamvu yao yalephera; akhala ngati akazi; nyumba zace zapsya ndi moto; akapici ace atyoka.

Yeremiya 51

Yeremiya 51:25-34