Yeremiya 50:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndakuchera iwe msampha, ndi iwenso wagwidwa, iwe Babulo, ndipo sunadziwa, wapezeka, ndiponso wagwidwa, cifukwa walimbana ndi Yehova.

Yeremiya 50

Yeremiya 50:21-31