Yeremiya 48:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Keroti walandidwa, ndi malinga agwidwa, ndipo tsiku lomwelo mtima wa anthu amphamvu a Moabu adzakhala ngati mtima wa mkazi alinkudwala.

Yeremiya 48

Yeremiya 48:34-47