Yeremiya 44:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti otsala a Yuda, amene ananka ku dziko la Aigupto kukhala m'menemo, asapulumuke asatsale ndi mmodzi yense, kuti abwere ku dziko la Yuda, kumene afuna kubwera kuti akhale m'menemo; pakuti adzabwera koma adzapulumuka ndiwo.

Yeremiya 44

Yeremiya 44:8-15