Yeremiya 4:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nenani m'Yuda, lalikirani m'Yerusalemu, ndi kuti, Ombani lipenga m'dzikomo; pfuulani, ndi kuti, Sonkhanani pamodzi, tilowe m'midzi ya malinga.

Yeremiya 4

Yeremiya 4:1-6