Yeremiya 38:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zedekiya analumbira m'tseri kwa Yeremiya, kuti, Pali Yehova, amene anatilengera ife moyo uno, sindidzakupha iwe sindidzakupereka iwe m'manja mwa anthu awa amene afuna moyo wako.

Yeremiya 38

Yeremiya 38:12-24