Yeremiya 37:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngakhale mukadakantha nkhondo yonse ya Akasidi akumenyana, nanu, ngakhale akadatsala olasidwa okha okha mwa iwo, koma iwowa akadauka yense m'hema wace ndi kutentha mudzi uwu ndi moto.

Yeremiya 37

Yeremiya 37:2-16