Yeremiya 36:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali, pamene Yehudi anawerenga masamba atatu pena anai, mfumu inawadula ndi kampeni ka mlembi, niwaponya m'moto wa m'nkhumbaliromo, mpaka mpukutu wonse unatha kupsa ndi moto wa m'nkhumbaliromo.

Yeremiya 36

Yeremiya 36:20-32