Yeremiya 34:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamene nkhondo ya mfumu ya ku Babulo inamenyana ndi Yerualemu, ndi midzi yonse ya Yuda imene inatsala, ndi Lakisi ndi Azeka; pakuti midzi ya Yuda yamalinga yotsala ndi imeneyi.

Yeremiya 34

Yeremiya 34:1-13