Yeremiya 29:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero: Aneneri anu ndi akuombeza anu amene akhala pakati panu, asakunyengeni inu, musamvere maloto anu amene mulotetsa.

Yeremiya 29

Yeremiya 29:6-13