Yeremiya 29:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wa makamu atero: Taonani, ndidzatuma pa iwo lupanga, ndi njala, ndi caola, ndipo ndidzayesa iwo onga nkhuyu zoola, zosadyeka, pokhala nzoipa.

Yeremiya 29

Yeremiya 29:10-27