Yeremiya 26:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Bwanji mwanenera m'dzina la Yehova, kuti, Nyumba iyi idzafanana ndi Silo, mudzi uwu udzakhala bwinja lopanda wokhalamo? Ndipo anthu onse anamsonkhanira Yeremiya m'nyumba ya Yehova.

Yeremiya 26

Yeremiya 26:1-16