Yeremiya 23:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo katundu wa Yehova simudzachulanso konse; pakuti mau a munthu adzakhala katundu wace; pakuti mwasokoneza mau a Mulungu wamoyo, Yehova wa makamu, Mulungu wathu.

Yeremiya 23

Yeremiya 23:27-40