Yeremiya 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati simudzamva mau amenewa, Ine ndilumbira, pali Ine mwini, ati Yehova, nyumba iyi idzakhala yabwinja.

Yeremiya 22

Yeremiya 22:1-6