Yeremiya 16:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndiponso mau a Mulungu anadza kwa ine, kuti,

2. Usatenge mkazi, usakhale ndi ana amuna ndi akazi m'malo muno.

3. Pakuti Yehova atero za ana amuna ndi za ana akazi akubadwa m'malo muno, ndi za amai anawabala iwo, ndi za atate ao anawabala iwo m'dziko muno:

Yeremiya 16