Yeremiya 14:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Mau a Yehova amene anadza kwa Yeremiya onena za cirala. Yuda alira, ndipo zipata zace zilefuka, zikhala pansi