Yeremiya 11:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace atero Yehova wa makamu, Taonani, ndidzalanga iwo; anyamata adzafa ndi lupanga; ana ao amuna ndi akazi adzafa ndi njala;

Yeremiya 11

Yeremiya 11:15-23