Yeremiya 10:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Gawo la Yakobo silifanana ndi iwo; pakuti iye ndiye analenga zonse; Israyeli ndiye mtundu wa colowa cace; dzina lace ndi Yehova wa makamu.

Yeremiya 10

Yeremiya 10:6-20