Rute 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taona, Boazi anafuma ku Betelehemu, nati kwa oceka, Yehova akhale nanu. Namyankha iwo, Yehova akudalitseni.

Rute 2

Rute 2:3-5