Oweruza 6:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova anatuma munthu mneneri kwa ana a Israyeli, nanena nao, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Ine ndinakukwezani kucokera m'Aigupto, ndi kukuturutsani m'nyumba ya ukapolo;

Oweruza 6

Oweruza 6:1-11