Nyimbo 6:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Bwenzi lako wapita kuti,Mkaziwe woposa kukongola?Bwenzi lako wapambukira kuti,Tikamfunefune pamodzi nawe?

2. Bwenzi langa watsikira kumunda kwace,Ku zitipula za mphoka, Kukadya kumunda kwace, ndi kuchera akakombo.

Nyimbo 6