Numeri 5:29-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Ici ndi cilamulo ca nsanje, pamene mkazi, pokhala naye mwamuna wace, ampatukira nadetsedwa;

30. kapena pamene mtima wansanje umgwira mwamuna, ndipo acitira mkazi wace nsanje; pamenepo aziika mkazi pamaso pa Yehova, ndipo wansembe amcitire cilamulo ici conse.

31. Mwamunayo ndiye wosacita mphulupulu, koma mkazi uyo asenze mphulupulu yace.

Numeri 5