Numeri 36:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Colamulira Yehova za ana akazi a Tselofekadi ndi ici, kuti, Akwatibwe nao amene afuna eni ace; komatu akwatibwe nao a banja la pfuko la makolo ao okha okha.

Numeri 36

Numeri 36:2-13