Numeri 34:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Wa pfuko la ana a Aseri, kalonga Ahihudi mwana wa Selomi.

28. Wa pfuko la ana a Nafitali, kalonga Pedaheli mwana wa Amihudi.

29. Iwo ndiwo amene Yehova analamulira agawire ana a Israyeli colowa cao m'dziko la Kanani.

Numeri 34