Numeri 33:19-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Nacokera ku Ritima, nayenda namanga m'Rimoni Perezi. Nacokera ku Rimoni Perezi, nayenda namanga m'Libina.