Numeri 33:15-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Ndipo anacokera ku Refidimu, nayenda namanga m'cipululu ca Sinai.

16. Nacokera ku cipululu ca Sinai, nayenda namanga m'Kibiroti Hatava.

17. Nacokera ku Kibiroti Hatava, nayenda namanga m'Hazeroti.

18. Nacokera ku Hazeroti, nayenda namanga m'Ritima.

19. Nacokera ku Ritima, nayenda namanga m'Rimoni Perezi.

20. Nacokera ku Rimoni Perezi, nayenda namanga m'Libina.

Numeri 33