Numeri 33:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Nacokera ku Nyanja Yofiira, nayenda namanga m'cipululu ca Sini.

12. Nacokera ku cipululu ca Sini, nayenda namanga m'Dofika.

13. Nacokera ku Dofika, nayenda namanga m'Alusi.

Numeri 33