Numeri 31:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ng'ombe zidafikira zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi cimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi awiri mphambu ziwiri.

Numeri 31

Numeri 31:29-46