Numeri 30:15-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Koma akazifafaniza atatha kuzimva; pamenepo adzasenza mphulupulu yace. Awa ndi malemba amene Yehova analamulira