Numeri 26:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana amuna a Simeoni monga mwa mabanja ao ndiwo: Nemueli, ndiye kholo la banja la Anemueli; Yamini, ndiye kholo la banja la Ayamini; Yakini, ndiye kholo la banja la Ayakini;

Numeri 26

Numeri 26:6-22