Numeri 14:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Anthu awa adzaleka liti kundinyoza? ndipo adzayamba liti kundikhulupirira, cinkana zizindikilo zonse ndinazicita pakati pao?

Numeri 14

Numeri 14:5-20