Numeri 10:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, Dzipangire malipenga awiri asiliva; uwasule mapangidwe ace; ucite nao poitana