Nehemiya 11:31-36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aiya, ndi pa Beteli ndi miraga yace,

32. pa Anatoti, Nobi, Ananiya,

33. Hazori, Rama, Gitaimu,

34. Hadidi, Zeboimu, Nebalati,

35. Lodi, ndi Ono, cigwa ca amisiri.

36. Ndi magawo a Levi anakhala ena ku Yuda, ndi ena ku Benjamini.

Nehemiya 11