Nahumu 3:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali kuti onse akupenyerera iwe adzakuthawa, nadzati, Nineve wapasuka, adzamlira maliro ndani? ndidzakufunira kuti akukutonthoza?

Nahumu 3

Nahumu 3:1-13