Mlaliki 4:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Citsiru cimanga manja ace, nicidya nyama yace yace.

6. Dzanja limodzi lodzala pali mtendere liposa manja awiri oti tho pali bvuto ndi kungosautsa mtima.

7. Pamenepo ndinabwera ndi kupenyera zacabe kunja kuno.

Mlaliki 4