Mlaliki 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinabweranso tsono ndi kupenyera nsautso zonse zimacitidwa kunja kuno; ndipo taona, misozi ya otsenderezedwa, koma analibe wakuwatonthoza; ndipo akuwatsendereza anali ndi mphamvu koma iwowa analibe wakuwatonthoza.

Mlaliki 4

Mlaliki 4:1-10