Mlaliki 10:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. utsiru ukhazikika pamwamba penipeni, ndipo olemera angokhala mwamanyazi.

7. Ndaona akapolo atakwera pa akavalo, ndi mafumu, alikuyenda pansi ngati akapolo.

8. Wokumba mbuna adzagwamo; ndipo woboola mpanda njoka idzamluma.

Mlaliki 10