Miyambi 9:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Nzeru yamanga nyumba yace,Yasema zoimiritsa zace zisanu ndi ziwiri;

2. Yaphera nyama yace, nisanganiza vinyo wace,Nilongosolanso pa gome lace.

Miyambi 9