Miyambi 7:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Alikupita pakhwalala pafupi ndi mphambano ya pa mkaziyo,Ndi kuyenda pa njira ya ku nyumba yace;

9. Pa madzulo kuli sisiro,Pakati pa usiku pali mdima,

10. Ndipo taona, mkaziyo anamcingamira,Atabvala zadama wocenjera mtima,

Miyambi 7