Miyambi 31:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Wofuna kufa umpatse cakumwa caukali,Ndi vinyo kwa owawa mtima; Amwe, narwale umphawi wace, Osakumbukiranso bvuto