Miyambi 31:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mau a Lemueli mfumu, uthenga umene amace anamphunzitsa.

2. Ciani mwananga, Ciani mwana wa mimba yanga?Ciani mwana wa zowinda zanga?

Miyambi 31