Miyambi 30:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani anakwera kumwamba natsikanso?Ndani wakundika nafumbata mphepo?Ndani wamanga madzi m'maraya ace?Ndani wakhazikitsa matsiriziro onse a dziko?Dzina lace ndani? dzina la mwanace ndani? kapena udziwa.

Miyambi 30

Miyambi 30:1-9